Aroma 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tiyeni tikhale ndi khalidwe loyenera+ ngati anthu amene akuchita zinthu masana. Tizipewa maphwando oipa,* kumwa mwauchidakwa,* chiwerewere, khalidwe lopanda manyazi,*+ mikangano ndiponso nsanje.+ 1 Akorinto 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 chifukwa mukuganizabe ngati anthu amʼdzikoli.*+ Nanga ngati mukuchitirana nsanje ndiponso kukangana nokhanokha, si ndiye kuti ndinu akuthupi+ ndipo mukuyenda ngati anthu a mʼdzikoli?
13 Tiyeni tikhale ndi khalidwe loyenera+ ngati anthu amene akuchita zinthu masana. Tizipewa maphwando oipa,* kumwa mwauchidakwa,* chiwerewere, khalidwe lopanda manyazi,*+ mikangano ndiponso nsanje.+
3 chifukwa mukuganizabe ngati anthu amʼdzikoli.*+ Nanga ngati mukuchitirana nsanje ndiponso kukangana nokhanokha, si ndiye kuti ndinu akuthupi+ ndipo mukuyenda ngati anthu a mʼdzikoli?