Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Usamayendeyende pakati pa anthu a mtundu wako nʼkumafalitsa miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.*+ Ine ndine Yehova. Miyambo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense amene amakhululuka* zolakwa akufunafuna chikondi,+Koma amene amangokhalira kulankhula za nkhani inayake amalekanitsa mabwenzi apamtima.+
16 Usamayendeyende pakati pa anthu a mtundu wako nʼkumafalitsa miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.*+ Ine ndine Yehova.
9 Aliyense amene amakhululuka* zolakwa akufunafuna chikondi,+Koma amene amangokhalira kulankhula za nkhani inayake amalekanitsa mabwenzi apamtima.+