1 Akorinto 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano ndikukudandaulirani abale, mʼdzina la Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti nonse muzilankhula mogwirizana ndipo pakati panu pasakhale kugawanika,+ koma mukhale ogwirizana kwambiri pokhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+ Afilipi 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukamachita zimenezi, mudzachititsa kuti chimwemwe changa chisefukire. Muzisonyeza kuti mumaganiza mofanana, muli ndi chikondi chofanana komanso kuti ndinu ogwirizana kwambiri ndipo maganizo anu ndi amodzi.+
10 Tsopano ndikukudandaulirani abale, mʼdzina la Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti nonse muzilankhula mogwirizana ndipo pakati panu pasakhale kugawanika,+ koma mukhale ogwirizana kwambiri pokhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+
2 Mukamachita zimenezi, mudzachititsa kuti chimwemwe changa chisefukire. Muzisonyeza kuti mumaganiza mofanana, muli ndi chikondi chofanana komanso kuti ndinu ogwirizana kwambiri ndipo maganizo anu ndi amodzi.+