Genesis 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Upange chingalawa pogwiritsa ntchito matabwa a mtengo wa mnjale.+ Uchigawe zipindazipinda ndipo uchimate ndi phula+ mkati ndi kunja komwe.
14 Upange chingalawa pogwiritsa ntchito matabwa a mtengo wa mnjale.+ Uchigawe zipindazipinda ndipo uchimate ndi phula+ mkati ndi kunja komwe.