1 Timoteyo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso amangokhala osachita kanthu nʼkumangoyendayenda mʼmakomo mwa anzawo. Kuwonjezera pa kumangokhala osachita kanthu, amakondanso miseche, kulowerera nkhani za eni+ komanso kulankhula zinthu zimene sayenera kulankhula. 1 Petulo 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi kupirira pamene mukumenyedwa chifukwa choti mwachimwa kuli ndi phindu lanji?+ Koma Mulungu amasangalala mukamapirira mavuto chifukwa choti mukuchita zabwino.+
13 Komanso amangokhala osachita kanthu nʼkumangoyendayenda mʼmakomo mwa anzawo. Kuwonjezera pa kumangokhala osachita kanthu, amakondanso miseche, kulowerera nkhani za eni+ komanso kulankhula zinthu zimene sayenera kulankhula.
20 Kodi kupirira pamene mukumenyedwa chifukwa choti mwachimwa kuli ndi phindu lanji?+ Koma Mulungu amasangalala mukamapirira mavuto chifukwa choti mukuchita zabwino.+