Aefeso 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Muzigonjerana+ poopa Khristu. Yakobo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma nzeru yochokera kumwamba, choyamba, ndi yoyera,+ kenako yamtendere,+ yololera,+ yokonzeka kumvera, yodzaza ndi chifundo ndi zipatso zabwino,+ yopanda tsankho,+ ndiponso yopanda chinyengo.+
17 Koma nzeru yochokera kumwamba, choyamba, ndi yoyera,+ kenako yamtendere,+ yololera,+ yokonzeka kumvera, yodzaza ndi chifundo ndi zipatso zabwino,+ yopanda tsankho,+ ndiponso yopanda chinyengo.+