Aefeso 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa chifukwa chimenechi, siyani kuchita zinthu ngati anthu opanda nzeru, koma pitirizani kuzindikira chifuniro cha Yehova.*+ 1 Petulo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma mapeto a zinthu zonse ayandikira. Choncho khalani oganiza bwino,+ ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera.+
17 Pa chifukwa chimenechi, siyani kuchita zinthu ngati anthu opanda nzeru, koma pitirizani kuzindikira chifuniro cha Yehova.*+
7 Koma mapeto a zinthu zonse ayandikira. Choncho khalani oganiza bwino,+ ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera.+