Tito 2:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ukhale chitsanzo pa ntchito zabwino mʼnjira iliyonse. Uziphunzitsa zolondola* ndipo uzisonyeza kuti ndiwe wopanda chibwana.+ 8 Mawu ako azikhala oyenera, omwe sangatsutsidwe,+ kuti otsutsa achite manyazi ndipo asapeze chifukwa chotinenera.+
7 Ukhale chitsanzo pa ntchito zabwino mʼnjira iliyonse. Uziphunzitsa zolondola* ndipo uzisonyeza kuti ndiwe wopanda chibwana.+ 8 Mawu ako azikhala oyenera, omwe sangatsutsidwe,+ kuti otsutsa achite manyazi ndipo asapeze chifukwa chotinenera.+