Salimo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova ndi Mʼbusa wanga.+ Sindidzasowa kanthu.+ Yesaya 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye adzasamalira* gulu la nkhosa zake ngati mʼbusa.+ Ndi dzanja lake, adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa,Ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake. Nkhosa zimene zikuyamwitsa adzazitsogolera mwachikondi.+
11 Iye adzasamalira* gulu la nkhosa zake ngati mʼbusa.+ Ndi dzanja lake, adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa,Ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake. Nkhosa zimene zikuyamwitsa adzazitsogolera mwachikondi.+