-
Yuda 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Anthuwa akamadya nanu pamaphwando amene mumachita kuti musonyezane chikondi,+ amakhala ngati miyala ikuluikulu yobisika mʼmadzi. Alinso ngati abusa amene amadzidyetsa okha mopanda mantha,+ mitambo yopanda madzi yotengekatengeka ndi mphepo,+ komanso ngati mitengo yopanda zipatso koma nyengo yake yobereka itatsala pangʼono kutha, yoferatu* ndiponso yoti yazulidwa.
-