8 Chomalizira abale, pitirizani kuganizira zinthu zilizonse zoona, zilizonse zofunika kwambiri, zilizonse zolungama, zilizonse zoyera, zilizonse zolimbikitsa chikondi, zilizonse zimene anthu amaziyamikira, khalidwe labwino lililonse komanso chilichonse chotamandika.+