1 Akorinto 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu aliyense wochita nawo mpikisano amakhala wodziletsa pa zinthu zonse. Anthu amachita zimenezo kuti akalandire nkhata yakumutu imene imawonongeka,+ koma ife, kuti tikapeze nkhata yakumutu yomwe singawonongeke.+ 2 Timoteyo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu. Koma ayenera kukhala wodekha kwa onse,+ woyenerera kuphunzitsa, wougwira mtima ena akamulakwira+
25 Munthu aliyense wochita nawo mpikisano amakhala wodziletsa pa zinthu zonse. Anthu amachita zimenezo kuti akalandire nkhata yakumutu imene imawonongeka,+ koma ife, kuti tikapeze nkhata yakumutu yomwe singawonongeke.+
24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu. Koma ayenera kukhala wodekha kwa onse,+ woyenerera kuphunzitsa, wougwira mtima ena akamulakwira+