Yohane 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo unakhalapo kudzera mwa iye ndipo moyowo unali kuwala kounikira anthu.+ Yohane 6:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Simoni Petulo anayankha kuti: “Ambuye, tingapitenso kwa ndani?+ Inu ndi amene muli ndi mawu othandiza munthu kuti adzapeze moyo wosatha.+
68 Simoni Petulo anayankha kuti: “Ambuye, tingapitenso kwa ndani?+ Inu ndi amene muli ndi mawu othandiza munthu kuti adzapeze moyo wosatha.+