Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa Mulungu anakonda kwambiri dziko moti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense womukhulupirira asawonongedwe koma akhale ndi moyo wosatha.+ Aroma 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Mulungu akutisonyeza chikondi chake, chifukwa pamene tinali ochimwa, Khristu anatifera.+ Aroma 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Popeza sanaumire ngakhale Mwana wake koma anamupereka mʼmalo mwa ife tonse,+ angalephere bwanji kutipatsanso mokoma mtima zinthu zina zonse pamodzi ndi Mwana wakeyo? 1 Yohane 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Umboni umene Mulungu anapereka ndi wakuti, iye anatipatsa moyo wosatha+ kudzera mwa Mwana wake.+
16 Chifukwa Mulungu anakonda kwambiri dziko moti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense womukhulupirira asawonongedwe koma akhale ndi moyo wosatha.+
32 Popeza sanaumire ngakhale Mwana wake koma anamupereka mʼmalo mwa ife tonse,+ angalephere bwanji kutipatsanso mokoma mtima zinthu zina zonse pamodzi ndi Mwana wakeyo?