Mateyu 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyangʼanitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo mumtima mwake.+ Aroma 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma valani Ambuye Yesu Khristu,+ ndipo musamakonzekere kuchita zimene thupi limalakalaka.+
28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyangʼanitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo mumtima mwake.+