Yohane 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndikuchita zimenezi kuti onsewa akhale amodzi+ ngati mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife nʼcholinga choti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.
21 Ndikuchita zimenezi kuti onsewa akhale amodzi+ ngati mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife nʼcholinga choti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.