Aroma 8:15, 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa simunalandire mzimu wa ukapolo woyambitsanso mantha, koma munalandira mzimu wakuti mukhale ana, umene timafuula nawo kuti: “Abba,* Atate!”+ 16 Mzimuwo umachitira umboni limodzi ndi mzimu wathu+ kuti ndife ana a Mulungu.+ Aefeso 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa anatisankhiratu+ kuti adzatitenga nʼkukhala ana ake+ kudzera mwa Yesu Khristu, mogwirizana ndi zimene zinamusangalatsa komanso zimene anafuna.+
15 Chifukwa simunalandire mzimu wa ukapolo woyambitsanso mantha, koma munalandira mzimu wakuti mukhale ana, umene timafuula nawo kuti: “Abba,* Atate!”+ 16 Mzimuwo umachitira umboni limodzi ndi mzimu wathu+ kuti ndife ana a Mulungu.+
5 Chifukwa anatisankhiratu+ kuti adzatitenga nʼkukhala ana ake+ kudzera mwa Yesu Khristu, mogwirizana ndi zimene zinamusangalatsa komanso zimene anafuna.+