1 Petulo 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Inuyo mwabadwanso mwatsopano+ kudzera mʼmawu a Mulungu+ wamoyo ndi wamuyaya. Simunabadwe kuchokera mumbewu yoti ikhoza kuwonongeka, koma mumbewu yomwe singawonongeke.+
23 Inuyo mwabadwanso mwatsopano+ kudzera mʼmawu a Mulungu+ wamoyo ndi wamuyaya. Simunabadwe kuchokera mumbewu yoti ikhoza kuwonongeka, koma mumbewu yomwe singawonongeke.+