-
Genesis 4:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Koma sanasangalale ndi Kaini komanso nsembe yake ngakhale pangʼono. Choncho Kaini anapsa mtima kwambiri ndipo nkhope yake inagwa chifukwa cha chisoni.
-