Salimo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,Sindinabise cholakwa changa.+ Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+ Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah) Miyambo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+Koma amene amawaulula nʼkuwasiya adzachitiridwa chifundo.+ Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe. Pemphero lopembedzera la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.*+
5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,Sindinabise cholakwa changa.+ Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+ Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah)
13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+Koma amene amawaulula nʼkuwasiya adzachitiridwa chifundo.+
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe. Pemphero lopembedzera la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.*+