2 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma tasiya zinthu zochititsa manyazi zochitikira mseri, ndipo sitikuyenda mwachinyengo kapena kupotoza mawu a Mulungu.+ Koma pochititsa choonadi kuti chidziwike, takhala chitsanzo chabwino kwa munthu* aliyense pamaso pa Mulungu.+ 3 Yohane 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinasangalala kwambiri abale atabwera nʼkundiuza za choonadi chomwe uli nacho, pamene ukupitiriza kuyenda mʼchoonadi.+
2 Koma tasiya zinthu zochititsa manyazi zochitikira mseri, ndipo sitikuyenda mwachinyengo kapena kupotoza mawu a Mulungu.+ Koma pochititsa choonadi kuti chidziwike, takhala chitsanzo chabwino kwa munthu* aliyense pamaso pa Mulungu.+
3 Ndinasangalala kwambiri abale atabwera nʼkundiuza za choonadi chomwe uli nacho, pamene ukupitiriza kuyenda mʼchoonadi.+