Aroma 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pokonda abale, muzikhala ndi chikondi chenicheni. Pa nkhani yosonyezana ulemu, muziyamba ndi inuyo.+ Afilipi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musamachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena chifukwa chodzikuza,+ koma modzichepetsa, muziona kuti ena amakuposani.+ Aheberi 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzimvera amene akukutsogolerani+ ndipo muziwagonjera+ chifukwa iwo amayangʼanira miyoyo yanu ndipo adzayankha mlandu.+ Muzichita zimenezi kuti azigwira ntchito yawo mosangalala osati modandaula, chifukwa akatero sizingakuyendereni bwino.
10 Pokonda abale, muzikhala ndi chikondi chenicheni. Pa nkhani yosonyezana ulemu, muziyamba ndi inuyo.+
3 Musamachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena chifukwa chodzikuza,+ koma modzichepetsa, muziona kuti ena amakuposani.+
17 Muzimvera amene akukutsogolerani+ ndipo muziwagonjera+ chifukwa iwo amayangʼanira miyoyo yanu ndipo adzayankha mlandu.+ Muzichita zimenezi kuti azigwira ntchito yawo mosangalala osati modandaula, chifukwa akatero sizingakuyendereni bwino.