Aroma 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mofanana ndi zimenezi, mzimu umatithandiza pa zimene tikulephera kuchita.+ Chifukwa vuto ndi lakuti sitidziwa zimene tikufunika kutchula popemphera, koma mzimu umachonderera mʼmalo mwathu ndi madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza. Aefeso 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene mukuchita zimenezi, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ pogwiritsa ntchito pemphero+ ndi pembedzero la mtundu uliwonse. Kuti muchite zimenezi khalani maso ndipo nthawi zonse muzipemphera mopembedzera mʼmalo mwa oyera onse.
26 Mofanana ndi zimenezi, mzimu umatithandiza pa zimene tikulephera kuchita.+ Chifukwa vuto ndi lakuti sitidziwa zimene tikufunika kutchula popemphera, koma mzimu umachonderera mʼmalo mwathu ndi madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza.
18 Pamene mukuchita zimenezi, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ pogwiritsa ntchito pemphero+ ndi pembedzero la mtundu uliwonse. Kuti muchite zimenezi khalani maso ndipo nthawi zonse muzipemphera mopembedzera mʼmalo mwa oyera onse.