Ezekieli 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene ndinkaona masomphenyawo, ndinaona kuti pambali pa akerubiwo panali mawilo 4. Pambali pa kerubi aliyense panali wilo limodzi ndipo mawilowo ankaoneka kuti akuwala ngati mwala wa kulusolito.+ Ezekieli 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mʼmatupi onse a akerubiwo, kumsana kwawo, mʼmanja mwawo, mʼmapiko awo ndiponso mʼmawilo a akerubi onse 4 munali maso paliponse.+
9 Pamene ndinkaona masomphenyawo, ndinaona kuti pambali pa akerubiwo panali mawilo 4. Pambali pa kerubi aliyense panali wilo limodzi ndipo mawilowo ankaoneka kuti akuwala ngati mwala wa kulusolito.+
12 Mʼmatupi onse a akerubiwo, kumsana kwawo, mʼmanja mwawo, mʼmapiko awo ndiponso mʼmawilo a akerubi onse 4 munali maso paliponse.+