4 Ine Yohane, ndikulembera mipingo 7+ imene ili mʼchigawo cha Asia:
Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere zikhale nanu kuchokera kwa “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera,”+ ndiponso kuchokera kwa mizimu 7+ imene ili pamaso pa mpando wake wachifumu.