7 Iye anachitiridwa zankhanza+ ndipo analola kuti azunzidwe,+
Koma sanatsegule pakamwa pake.
Anamutengera kumalo oti akamuphere ngati nkhosa,+
Mofanana ndi nkhosa yaikazi imene yangokhala chete pamene akufuna kuimeta ubweya,
Ndipo sanatsegule pakamwa pake.+