Chivumbulutso 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho amene wapambana pankhondo+ adzavekedwa zovala zoyera+ ndipo sindidzafufuta dzina lake mʼbuku la moyo.+ Koma ndidzavomereza dzina lake pamaso pa Atate wanga ndi pamaso pa angelo ake.+
5 Choncho amene wapambana pankhondo+ adzavekedwa zovala zoyera+ ndipo sindidzafufuta dzina lake mʼbuku la moyo.+ Koma ndidzavomereza dzina lake pamaso pa Atate wanga ndi pamaso pa angelo ake.+