1Ine Paulo, mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, ndine mtumwi wa Khristu Yesu ndipo ndikulembera oyera amene ali ku Efeso,+ amene ndi ophunzira a Khristu Yesu okhulupirika kuti:
2“Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Efeso+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena wonyamula nyenyezi 7 mʼdzanja lake lamanja, amene akuyenda pakati pa zoikapo nyale 7 zagolide:+