Salimo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, ndi ndani amene angakhale mlendo mutenti yanu? Ndi ndani amene angakhale mʼphiri lanu lopatulika?+ Chivumbulutso 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu akuti: “Taonani! Chihema cha Mulungu chili pakati pa anthu ndipo iye azidzakhala nawo. Iwo adzakhala anthu ake ndipo Mulunguyo adzakhala nawo.+
15 Inu Yehova, ndi ndani amene angakhale mlendo mutenti yanu? Ndi ndani amene angakhale mʼphiri lanu lopatulika?+
3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu akuti: “Taonani! Chihema cha Mulungu chili pakati pa anthu ndipo iye azidzakhala nawo. Iwo adzakhala anthu ake ndipo Mulunguyo adzakhala nawo.+