Chivumbulutso 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika+ akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo wa Mulunguzo padziko lapansi.”+ Chivumbulutso 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mngelo wa 4 anathira mbale yake padzuwa+ ndipo dzuwalo linaloledwa kuwotcha anthu ndi moto.
16 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika+ akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo wa Mulunguzo padziko lapansi.”+