Chivumbulutso 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Tiyatira+ lemba kuti: Izi ndi zimene Mwana wa Mulungu akunena, iye amene maso ake ali ngati lawi la moto+ ndipo mapazi ake ali ngati kopa* woyengedwa bwino:+
18 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Tiyatira+ lemba kuti: Izi ndi zimene Mwana wa Mulungu akunena, iye amene maso ake ali ngati lawi la moto+ ndipo mapazi ake ali ngati kopa* woyengedwa bwino:+