Chivumbulutso 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma mmodzi wa akulu aja anandiuza kuti: “Tonthola. Taona! Mkango wa fuko la Yuda,+ muzu+ wa Davide,+ anapambana pankhondo+ moti ndi woyenera kumatula zidindo 7 zimene amatira mpukutuwo nʼkuutsegula.”
5 Koma mmodzi wa akulu aja anandiuza kuti: “Tonthola. Taona! Mkango wa fuko la Yuda,+ muzu+ wa Davide,+ anapambana pankhondo+ moti ndi woyenera kumatula zidindo 7 zimene amatira mpukutuwo nʼkuutsegula.”