Salimo 90:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mapiri asanabadwe,Kapena musanakhazikitse dziko lapansi komanso nthaka,+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+ Chivumbulutso 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nthawi zonse angelowo akamapereka ulemerero ndi ulemu ndiponso akamayamikira Mulungu amene wakhala pampando wachifumuyo, Amene adzakhale ndi moyo kwamuyaya,+
2 Mapiri asanabadwe,Kapena musanakhazikitse dziko lapansi komanso nthaka,+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+
9 Nthawi zonse angelowo akamapereka ulemerero ndi ulemu ndiponso akamayamikira Mulungu amene wakhala pampando wachifumuyo, Amene adzakhale ndi moyo kwamuyaya,+