Salimo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amakonda kwambiri chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kuganizira mozama* chilamulocho masana ndi usiku.+ Luka 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma iye ananena kuti: “Ayi, mʼmalomwake, osangalala ndi anthu amene akumva mawu a Mulungu nʼkuwasunga!”+ Yohane 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati zimenezi mukuzidziwa, mudzakhala osangalala mukamazichita.+ Yakobo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, nʼkumadzipusitsa ndi maganizo abodza.
2 Koma amakonda kwambiri chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kuganizira mozama* chilamulocho masana ndi usiku.+
28 Koma iye ananena kuti: “Ayi, mʼmalomwake, osangalala ndi anthu amene akumva mawu a Mulungu nʼkuwasunga!”+
22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, nʼkumadzipusitsa ndi maganizo abodza.