Chivumbulutso 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+
15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+