-
Yohane 8:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Inu ndinu ochokera kwa atate wanu Mdyerekezi, ndipo mukufuna kuchita zimene atate wanu amafuna.+ Iye ndi wopha anthu kuchokera pachiyambi+ ndipo sanapitirize kukhala mʼchoonadi, chifukwa mwa iye mulibe choonadi. Akamanena bodza, amangosonyeza mmene alili, chifukwa iye ndi wabodza komanso tate wake wa bodza.+
-