1 Yohane 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikulembera inu abambo chifukwa mukumudziwa iye amene wakhalapo kuyambira pachiyambi. Ndikulembera inu anyamata chifukwa ndinu olimba+ ndipo mumakhulupirira mawu a Mulungu+ komanso mwagonjetsa woipayo.+
14 Ndikulembera inu abambo chifukwa mukumudziwa iye amene wakhalapo kuyambira pachiyambi. Ndikulembera inu anyamata chifukwa ndinu olimba+ ndipo mumakhulupirira mawu a Mulungu+ komanso mwagonjetsa woipayo.+