Chivumbulutso 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno chinjokacho chinangoima pamchenga wamʼmbali mwa nyanja. Kenako ndinaona chilombo+ chikutuluka mʼnyanja.+ Chinali ndi nyanga 10 ndi mitu 7. Panyanga yake iliyonse panali chisoti chachifumu. Koma pamitu yake panali mayina onyoza Mulungu.
13 Ndiyeno chinjokacho chinangoima pamchenga wamʼmbali mwa nyanja. Kenako ndinaona chilombo+ chikutuluka mʼnyanja.+ Chinali ndi nyanga 10 ndi mitu 7. Panyanga yake iliyonse panali chisoti chachifumu. Koma pamitu yake panali mayina onyoza Mulungu.