Yeremiya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake. 1 Timoteyo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kwa Mulungu yekhayo+ yemwe ndi Mfumu yamuyaya,+ amene saafa+ komanso wosaoneka,+ kukhale ulemu ndi ulemerero mpaka kalekale. Ame.
10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake.
17 Kwa Mulungu yekhayo+ yemwe ndi Mfumu yamuyaya,+ amene saafa+ komanso wosaoneka,+ kukhale ulemu ndi ulemerero mpaka kalekale. Ame.