Yeremiya 51:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Iwe mkazi amene ukukhala pamadzi ambiri,+Amene uli ndi chuma chambiri,+Mapeto ako afika ndipo nthawi yako yopanga phindu yatha.+ Chivumbulutso 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo uja anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, magulu a anthu, mayiko komanso zilankhulo.+ Chivumbulutso 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi chiwerewere* chake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”*+
13 “Iwe mkazi amene ukukhala pamadzi ambiri,+Amene uli ndi chuma chambiri,+Mapeto ako afika ndipo nthawi yako yopanga phindu yatha.+
15 Mngelo uja anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, magulu a anthu, mayiko komanso zilankhulo.+
2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi chiwerewere* chake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”*+