Yesaya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taonani zimene zikubwera: Kukubwera amuna amene akwera galeta lankhondo limene likukokedwa ndi mahatchi awiri.”+ Kenako iye analankhula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+ Yeremiya 51:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Babulo wagwa mwadzidzidzi ndipo wasweka.+ Mulirireni mofuula.+ Mʼpatseni mafuta a basamu kuti ululu wake uthe, mwina angachire.” Chivumbulutso 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako mngelo wachiwiri anamutsatira ndipo anati: “Wagwa! Babulo Wamkulu+ wagwa,+ amene anachititsa kuti mitundu yonse ya anthu imwe vinyo wa chilakolako cha* chiwerewere* chake!”+
9 Taonani zimene zikubwera: Kukubwera amuna amene akwera galeta lankhondo limene likukokedwa ndi mahatchi awiri.”+ Kenako iye analankhula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+
8 Babulo wagwa mwadzidzidzi ndipo wasweka.+ Mulirireni mofuula.+ Mʼpatseni mafuta a basamu kuti ululu wake uthe, mwina angachire.”
8 Kenako mngelo wachiwiri anamutsatira ndipo anati: “Wagwa! Babulo Wamkulu+ wagwa,+ amene anachititsa kuti mitundu yonse ya anthu imwe vinyo wa chilakolako cha* chiwerewere* chake!”+