Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+ Yeremiya 51:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 “Babulo sanaphetse anthu a mu Isiraeli okha+Koma anaphetsanso anthu apadziko lonse lapansi ku Babuloko.
6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+
49 “Babulo sanaphetse anthu a mu Isiraeli okha+Koma anaphetsanso anthu apadziko lonse lapansi ku Babuloko.