Ekisodo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+
3 Ndinkaonekera kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse kwa iwo.+