17 chifukwa Mwanawankhosa,+ amene ali pambali* pa mpando wachifumu, adzawaweta+ nʼkuwatsogolera ku akasupe a madzi a moyo.+ Ndipo Mulungu adzapukuta misozi yonse mʼmaso mwawo.”+
22Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu ndi wa Mwanawankhosa.+