Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la 1 Atesalonika 1 ATESALONIKA ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Moni (1) Kuthokoza chifukwa cha chikhulupiriro cha Atesalonika (2-10) 2 Utumiki wa Paulo ku Tesalonika (1-12) Atesalonika analandira mawu a Mulungu (13-16) Paulo ankalakalaka kuona Atesalonika (17-20) 3 Paulo anapitiriza kukhala ku Atene podikira lipoti lochokera ku Tesalonika (1-5) Timoteyo anabweretsa lipoti lolimbikitsa (6-10) Anapempherera Atesalonika (11-13) 4 Anawachenjeza kuti azipewa chiwerewere (1-8) Muzikondana kwambiri kuposa mmene mukuchitira (9-12) “Musamalowerere nkhani za ena” (11) Amene anafa mwa Khristu adzakhala oyambirira kuuka (13-18) 5 Kubwera kwa tsiku la Yehova (1-5) “Bata ndi mtendere!” (3) Khalanibe maso komanso oganiza bwino (6-11) Kuwalimbikitsa (12-24) Moni womaliza (25-28)