Kumasuka ku Mantha Kwayandikira!
NGAKHALE kuti munthu amakhala m’mantha kwa moyo wake wonse, tingayang’ane mwachidaliro ku nthaŵi ina patsogolopa pamene Ufumu wa Mulungu mwa Kristu Yesu udzachotsa kotheratu kuvutika konse—kuphatikizapo matenda ndi imfa. Magazini ano asonyeza zimene zifunikira kuti mupindule ndi makonzedwe achikondi a Mulungu. Ngati mungafune chidziŵitso chowonjezereka kapena kuti wina akufikireni kudzachititsa phunziro la Baibulo lapanyumba laulere kwa inu, chonde lemberani ku Watch Tower, Box 33459, Lusaka 10101, kapena ku keyala yoyenerera yondandalikidwa patsamba 2.