December 14-20
LEVITIKO 12-13
Nyimbo Na. 140 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Tingaphunzire pa Malamulo Okhudza Khate”: (10 min.)
Le 13:4, 5—Anthu odwala khate ankaikidwa kwaokha (wp18.1 7)
Le 13:45, 46—Akhate ankayenera kupewa kupatsira ena (wp16.4 9 ¶1)
Le 13:52, 57—Zinthu zimene zadetsedwa zinkafunika kuwonongedwa (it-2 238 ¶3)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Le 12:2, 5—N’chifukwa chiyani mayi ankakhala wodetsedwa akabereka mwana? (w04 5/15 23 ¶2)
Le 12:3—Kodi n’chiyani chimene chiyenera kuti chinachititsa Yehova kulamula kuti ana aamuna azidulidwa akakwanitsa masiku 8 atabadwa? (wp18.1 7)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 13:9-28 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (4 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso akuti: Kodi Tony anagwiritsa ntchito bwanji mafunso mwanzeru? Kodi anathandiza bwanji munthuyo kumvetsa mfundo yamulembalo?
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 19)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako musonyezeni kabuku ka Uthenga Wabwino n’kuyamba kuphunzira naye phunziro 11. (th phunziro 9)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 112
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 143 ndi Pemphero