NUMERI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-
Msasa anaugawa mʼmagulu a mafuko atatu (1-34)
Gulu la mafuko atatu la Yuda linali mbali yakumʼmawa (3-9)
Gulu la mafuko atatu la Rubeni linali mbali yakumʼmwera (10-16)
Msasa wa Alevi unali pakati (17)
Gulu la mafuko atatu la Efuraimu linali mbali yakumadzulo (18-24)
Gulu la mafuko atatu la Dani linali mbali yakumpoto (25-31)
Chiwerengero cha amuna onse amene analembedwa (32-34)
-
Nsembe zimene anapereka pa mwambo wotsegulira chihema (1-89)
-
Mulungu anawabweretsera moto chifukwa chodandaula (1-3)
Anthu anayamba kulirira nyama (4-9)
Mose ankadziona kuti ndi wosayenerera (10-15)
Yehova anapereka mzimu kwa akulu 70 (16-25)
Eledadi ndi Medadi; Yoswa anachita nsanje chifukwa choti ankadera nkhawa Mose (26-30)
Anabweretsa zinziri; anthu analangidwa chifukwa cha dyera (31-35)
-
Ndodo ya Aroni inachita maluwa monga chizindikiro (1-13)
-
Ngʼombe yofiira komanso madzi oyeretsera (1-22)
-
Kalembera wachiwiri wa mafuko a Isiraeli (1-65)
-
Anayamba kukhala kumʼmawa kwa Yorodano (1-42)
-
Lamulo lokhudza ukwati wa akazi amene akulandira cholowa (1-13)