Genesis 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Anthu awa akufuna kuti tizikhala nawo mwamtendere. Ndiye aloleni akhale mʼdzikoli nʼkumachita malonda, popeza dzikoli ndi lalikulu moti atha kukhalamo. Tikhoza kukwatira ana awo aakazi ndiponso tikhoza kuwapatsa ana athu aakazi.+
21 “Anthu awa akufuna kuti tizikhala nawo mwamtendere. Ndiye aloleni akhale mʼdzikoli nʼkumachita malonda, popeza dzikoli ndi lalikulu moti atha kukhalamo. Tikhoza kukwatira ana awo aakazi ndiponso tikhoza kuwapatsa ana athu aakazi.+