Genesis 39:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Yehova anali ndi Yosefe,+ moti chilichonse chimene ankachita chinkamuyendera bwino. Ndipo anaikidwa kuti aziyangʼanira nyumba ya munthu wa ku Iguputo uja, amene anali mbuye wake.
2 Koma Yehova anali ndi Yosefe,+ moti chilichonse chimene ankachita chinkamuyendera bwino. Ndipo anaikidwa kuti aziyangʼanira nyumba ya munthu wa ku Iguputo uja, amene anali mbuye wake.